Danieli 2:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

kuti apemphe zacifundo kwa Mulungu wa Kumwamba pa cinsinsi ici; kuti Danieli ndi anzace asaonongeke pamodzi ndi eni nzeru ena a ku Babulo.

Danieli 2

Danieli 2:15-21