Danieli 11:43 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo adzacita mwamphamvu ndi cuma ca golidi, ndi siliva, ndi zinthu zofunika zonse za Aigupto; Alubi ndi Akusi adzatsata mapazi ace.

Danieli 11

Danieli 11:34-45