Danieli 11:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mafumu awa onse awiri mitima yao idzakumbuka kucita zoipa, nadzanena bodza ali pa gome limodzi; koma osapindula nalo; pakuti kutha kwace kudzakhala pa nthawi yoikika.

Danieli 11

Danieli 11:22-29