Danieli 11:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Adzafika kacetecete ku minda yokometsetsa ya derali, nadzacita cosacita atate ace, kapena makolo ace; adzawawazira zofunkha, ndi zankhondo, ndi cuma, nadzalingiririra malinga ziwembu zace; adzatero nthawi.

Danieli 11

Danieli 11:19-32