Danieli 11:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi mfumu ya kumpoto idzadza, nidzaunda mtumbira, nidzalanda midzi yamalinga; ndi ankhondo a kumwela sadzalimbika, ngakhale anthu ace osankhika; inde sipadzakhala mphamvu yakulimbika.

Danieli 11

Danieli 11:10-19