Danieli 10:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ine Danieli ndekha ndinaona masomphenyawo; pakuti anthu anali nane sanaona masomphenyawo; koma kunawagwera kunjenjemera kwakukuru, nathawa kubisala.

Danieli 10

Danieli 10:4-15