Danieli 10:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo tsiku la makumi awiri mphambu anai la mwezi woyamba, pokhala ine m'mphepete mwa mtsinje waukuru, ndiwo Hidikeli,

Danieli 10

Danieli 10:2-14