Danieli 10:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti mnyamata wa mbuye wanga inu akhoza bwanji kulankhula ndi mbuye wanga inu? pakuti ine tsopano apa mulibenso mphamvu mwa ine, osanditsaliranso mpweya.

Danieli 10

Danieli 10:15-21