Danieli 10:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo anati kwa ine, Usaope Danieli; pakuti kuyambira tsiku loyamba lija unaika mtima wako kuzindikira ndi kudzicepetsa pamaso pa Mulungu wako, mau ako anamveka; ndipo ndadzera mau ako,

Danieli 10

Danieli 10:3-21