Danieli 1:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Danieli anatsimikiza mtimti kuti asadzidetse ndi cakudya ca mfumu, kapena ndi vinyo amamwa; cifukwa cace anapempha mkuru wa adindo amlole asadzidetse.

Danieli 1

Danieli 1:1-17