Cibvumbulutso 8:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndinaona, ndipo ndinamva ciombankhanga cirikuuluka pakati pa mwamba, ndi kunena ndi mau akuru, Tsoka, tsoka, tsoka, iwo akukhala padz'ko, cifukwa ca mau otsala a lipenga la angelo atatu asanaombe.

Cibvumbulutso 8

Cibvumbulutso 8:12-13