Cibvumbulutso 7:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndinaona mngelo wina, anakwera kucokera poturuka dzuwa, ali naco cizindikilo ca Mulungu wamoyo: ndipo anapfuula ndi mau akuru kuitana angelo anai, amene adalandira mphamvu kuipsa dziko ndi nyanja,

Cibvumbulutso 7

Cibvumbulutso 7:1-9