Cibvumbulutso 6:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamene anamasula cizindikilo cacitatu, ndinamva camoyo cacitatu nicinena, Idza. Ndipo ndinapenya, taonani, kavalo wakuda; ndipo iye womkwera anali nao muyeso m'dzanja lace.

Cibvumbulutso 6

Cibvumbulutso 6:1-15