Cibvumbulutso 6:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo anapfuula ndi mau akulu, ndi kunena, Kufikira liti, Mfumu yoyera ndi yoona, muleka kuweruza ndi kubwezera cilango cifukwa ca mwazi wathu, pa iwo akukhala padziko?

Cibvumbulutso 6

Cibvumbulutso 6:1-12