Cibvumbulutso 6:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndinaona pamene Mwanawankhosa anamasula cimodzi ca zizindikilo zisanu ndi ziwiri, ndipo ndinamva cimodzi mwa zamoyo zinai, nicinena, ngati mau a bingu, Idza.

Cibvumbulutso 6

Cibvumbulutso 6:1-3