Cibvumbulutso 5:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndinaona, ndipo ndinamva mau a angelo ambiri pozinga mpando wacifumu, ndi zamoyo ndi akulu; ndipo mawerengedwe ao anali zikwi khumi kucurukitsa zikwi khumi ndi zikwiza zikwi;

Cibvumbulutso 5

Cibvumbulutso 5:8-14