Cibvumbulutso 4:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Zitatha izi ndinapenya, ndipo taonani, khomo lotseguka m'Mwamba, ndipo mau oyamba ndinawamva, ngati lipenga Iakulankhuia ndi ine, anati, Kwera kuno, ndipo ndidzakuonetsa zimene ziyenera kucitika m'tsogolomo.

Cibvumbulutso 4

Cibvumbulutso 4:1-4