Cibvumbulutso 3:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Iye amene alakika adzambveka motero zobvala zoyera; ndipo sindidzafafaniza ndithu dzina lace m'buku la moyo, ndipo ndidzambvomereza dzina lace pamaso pa Atate wanga, ndi pamaso pa angelo ace.

Cibvumbulutso 3

Cibvumbulutso 3:1-15