Cibvumbulutso 22:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Odala iwo amene atsuka miinjiro yao, kuti akakhale nao ulamuliro pa mtengo wa moyo, ndi kuti akalowe m'mzinda pazipata.

Cibvumbulutso 22

Cibvumbulutso 22:12-19