Cibvumbulutso 21:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndinamva mau akuru ocokera ku mpando wacifumu, ndi kunena Taonani, cihema ca Mulungu ciri mwa anthu; ndipo adzakhalitsa nao, ndi iwo adzakhala anthu ace, ndi Mulungu yekha adzakhala nao, Mulungu wao;

Cibvumbulutso 21

Cibvumbulutso 21:1-11