Cibvumbulutso 21:24-26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

24. Ndipo 2 amitundu adzayendayenda mwa kuunika kwace; ndi mafumu a dziko atenga ulemerero wao kulowa nao momwemo.

25. Ndipo 3 pa zipata zace sipatsekedwa konse usana, 4 (pakuti sikudzakhala usiku komweko);

26. ndipo 5 adzatenga ulemerero ndi ulemu wa amitundu nadzalowa nao momwemo;

Cibvumbulutso 21