Cibvumbulutso 20:14-15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

14. Ndipo imfa ndi Hade zinaponyedwa m'nyanja yamoto. Iyo ndiyo imfa yaciwiri, ndiyo nyanja yamoto.

15. Ndipo ngati munthu sanapezedwa wolembedwa m'buku la moyo, anaponyedwa m'nyanja yamoto.

Cibvumbulutso 20