Cibvumbulutso 20:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndinaona, mpando wacifumu waukuru woyera, ndi iye wakukhalapo, amene dziko ndi m'mwamba zinathawa pamaso pace, ndipo sanapezedwamalo ao.

Cibvumbulutso 20

Cibvumbulutso 20:8-15