Cibvumbulutso 2:27-29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

27. ndipo 7 adzawalamulira ndi ndodo yacitsulo, monga zotengera za woumba mbiya ziphwanyika mapale; monga lnenso ndalandira kwa Atate wanga;

28. ndipo ndidzampatsa iye 8 nthanda.

29. Iye wokhala nalo khutu amve cimene Mzimu anena kwa Mipingo.

Cibvumbulutso 2