Cibvumbulutso 2:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma ndinena kwa inu, kwa otsala a ku Tiyatira, onse amene alibe ciphunzitso ici, amene sanazindikira zakuya za Satana, monga anena, Sindikusanjikizani katundu wina.

Cibvumbulutso 2

Cibvumbulutso 2:21-29