Cibvumbulutso 2:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kwa mngelo wa Mpingo wa ku Tiyatira lemba:Izi azinena Mwana wa Mulungu, wakukhala nao maso ace ngati lawi la moto, ndi mapazi ace ngati mkuwa wonyezimira:

Cibvumbulutso 2

Cibvumbulutso 2:15-21