Cibvumbulutso 2:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndidziwa kumene ukhalako kuja kuli mpando wacifumu wa Satana; ndipo ugwira dzina langa, osakaniza cikhulupiriro canga, angakhale m'masiku a Antipa, mboni yanga, wokhulupirika wanga, amene anaphedwa pali inu, kuja akhalako Satana.

Cibvumbulutso 2

Cibvumbulutso 2:12-20