Cibvumbulutso 19:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

pakuti maweruzo ace ali oona ndi olungama; ndipo anaweruza mkazi wacigololo wamkuru, amene anaipsa dziko ndi cigololo cace, ndipo anabwezera cilango mwazi wa akapolo ace pa dzanja lace la mkaziyo.

Cibvumbulutso 19

Cibvumbulutso 19:1-5