Cibvumbulutso 18:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti m'ora limodzi casanduka bwinja cuma cacikuru cotere. Ndipo watsigiro ali yense, ndi yense wakupita panyanja pakuti pakuti, ndi amarinyero, ndi onse amene amacita kunyanja, anaima patali,

Cibvumbulutso 18

Cibvumbulutso 18:9-21