Cibvumbulutso 17:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo nyanga khumi udaziona, ndi cirombo, izi zidzadana ndi mkazi wacigololoyo, nizidzamkhalitsa wabwinja wausiwa, nizidzadya nyama yace, nizidzampsereza ndi moto.

Cibvumbulutso 17

Cibvumbulutso 17:12-18