Cibvumbulutso 17:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anadza mmodzi mwa angelo asanu ndi awiri akukhala nazo mbale zisanu ndi ziwiri, nalankhula ndi ine, nanena, Idza kuno, ndidzakuonetsa citsutso ca mkazi wacigololo wamkuru, wakukhala pa madzi ambiri,

Cibvumbulutso 17

Cibvumbulutso 17:1-6