Cibvumbulutso 14:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndinaona mngelo wina alikuuluka pakati pa mlengalenga, wakukhala nao Uthenga Wabwino wosatha, aulalikire kwa iwo akukhala padziko, ndi kwa mtundu uti wonse ndi pfuko ndi manenedwe ndi anthu j

Cibvumbulutso 14

Cibvumbulutso 14:1-7