Cibvumbulutso 13:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anacipatsa ico m'kamwa molankhula zazikuru ndi zamwano; ndipo anacipatsa ulamuliro wa kutero miyezi makumi anai ndi iwiri.

Cibvumbulutso 13

Cibvumbulutso 13:1-10