Cibvumbulutso 13:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndinaimirira pa mcenga wa nyanja.Ndipo ndinaona cirombo cirinkuturuka m'nyanja, cakukhala nazo nyanga khumi, ndi mitu isanu ow iwiri, ndi pa nyanga zace nduwira zacifumu khumi, ndi pamitu pace maina a mwano.

Cibvumbulutso 13

Cibvumbulutso 13:1-2