Cibvumbulutso 12:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mkazi anathawira kucipululu, kumene ali nayo mbuto yokonzekeratu ndi Mulungu, kuti kumeneko akamdyetse masiku cikwi cimodzi ndi mazana awiri mphambu makumi asanu ndi limodzi.

Cibvumbulutso 12

Cibvumbulutso 12:1-12