Cibvumbulutso 12:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo cinaoneka cizindikilo cina m'mwamba, taonani, cinjoka cofiira, cacikuru, cakukhala nayo mitu isanu ndi iwiri, ndi nyanga khumi, ndi pamutu pace nduwira zacifumu zisanu ndi ziwiri.

Cibvumbulutso 12

Cibvumbulutso 12:1-12