Cibvumbulutso 12:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndinamva mau akuru m'Mwamba, nanena, Tsopano zafika cipulumutso, ndi mphamvu, ndi ufumu za Mulungu wathu, ndi ulamuliro wa Kristu wace; pakuti wagwetsedwa wonenera wa abale athu, wakuwanenera pamaso pa Mulungu wathu usana ndi usiku.

Cibvumbulutso 12

Cibvumbulutso 12:2-17