Cibvumbulutso 12:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo cizindikilo cacikuru cinaoneka m'mwamba; mkazi wobvekedwa dzuwa, ndi mwezi ku mapazi ace, ndi pamutu pace korona wa nyenyezi khumi ndi ziwiri;

Cibvumbulutso 12

Cibvumbulutso 12:1-4