Cibvumbulutso 11:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mitembo yao idzakhala pa khwalala la mudzi waukuru, umene uchedwa, ponena zacizimu, Sodoma ndi Aigupto, pameneponso Ambuye wao anapacikidwa.

Cibvumbulutso 11

Cibvumbulutso 11:1-18