Cibvumbulutso 11:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndidzalamulira mboni zanga ziwiri, ndipo zidzanenera masiku cikwi cimodzi ndi mazana awiri mphambu makumi asanu ndi limodzi, zobvala ciguduli.

Cibvumbulutso 11

Cibvumbulutso 11:1-7