Cibvumbulutso 11:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo amitundu anakwiya, ndipo unadza mkwiyo wanu, ndi nthawi ya akufa yakuti aweruzidwe, ndi yakupereka mphotho akapolo anu aneneriwo, ndi oyera mtima, ndi iwo akuopa dzina lanu, ang'ono ndi akuru; ndi kuononga iwo akuononga dziko.

Cibvumbulutso 11

Cibvumbulutso 11:12-19