Cibvumbulutso 10:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamene adalankhula mabingu asanu ndi awiriwo, ndinati ndilembe; ndipo udinamva mau ocokera Kumwamba nanena, Sindikiza naco cizindikilo zimene adalankhula mabingu asanu ndi limodzi, ndipo usazilembe,

Cibvumbulutso 10

Cibvumbulutso 10:1-11