Cibvumbulutso 10:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndinaona mngelo wina wolimba alikutsika Kumwamba, wobvala mtambo; ndi utawaleza pamutu pace, ndi nkhope yace ngati dzuwa, ndi mapazi ace ngati mizati yamoto;

Cibvumbulutso 10

Cibvumbulutso 10:1-10