Aroma 9:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti lembo linena kwa Farao, Cifukwa ca ici, ndinakuutsa iwe, kuti ndikaonetse mwa iwe mphamvu yanga, ndi kuti dzina langa likabukitsidwe pa dziko lonse lapansi.

Aroma 9

Aroma 9:7-26