Aroma 8:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo tidziwa kuti amene akonda Mulungu zinthu zonse zithandizana kuwacitira ubwino, ndiwo amene aitanidwa monga mwa kutsimikiza kwa mtima wace.

Aroma 8

Aroma 8:24-34