Aroma 8:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti ife tinapolumutsidwa ndi ciyembekezo; koma ciyembekezo cimene cioneka si ciri ciyembekezo ai; pa kuti ayembekezera ndani cimene acipenya?

Aroma 8

Aroma 8:19-34