Aroma 7:24-25 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Munthu wosauka ine; adzandilanditsa ndani m'thupi la imfa iyi? Ndiyamika Mulungu, mwa Yesu Kristu Ambuye wathu