Aroma 7:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti mkazi wokwatidwa amangidwa ndi lamulo kwa mwamuna wace wamoyo; koma mwamunayo akafa, iye amasulidwa ku lamulo la mwamunayo.

Aroma 7

Aroma 7:1-10