Aroma 6:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace tinaikldwa m'manda pamodzi ndi iye mwa ubatizo kulowa muimfa; kuti monga Kristu anaukitsidwa kwa akufa mwa ulemerero wa Atate, cotero ifenso tikayende m'moyo watsopano.

Aroma 6

Aroma 6:1-7