Aroma 6:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma tsopano, pamene munamasulidwa kuucimo, ndi kukhala akapolo a Mulungu, muli naco cobala canu cakufikira ciyeretso, ndi cimariziro cace moyo wosatha.

Aroma 6

Aroma 6:16-23